
Whatsapp
12m 10sKugwiritsa ntchito WhatsApp mmodzi kuma phone awiri ali kotalikana
By Kamlanje Tech
Mutu wa “Kugwiritsa ntchito WhatsApp account imodzi kuma phone awiri ali kotalikana” kuphunzitsa anthu mmene angagwiritsire ntchito akaunti imodzi ya WhatsApp pa mafoni awiri osakhala pamalo amodzi. Mwachitsanzo, munthu ali ndi phone yake yoyamba yomwe WhatsApp account ili, ndipo akufuna kulumikiza phone yachiwiri yomwe ili kwina kuti azitha kuwona ndi kutumiza mauthenga pa akaunti yomweyo.
